Ezekieli 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ‘Koma unayamba kudalira kukongola kwako+ ndipo unakhala hule chifukwa cha kutchuka kwako.+ Unayamba kuchita uhule mosadziletsa ndi munthu aliyense wodutsa mʼnjira+ ndipo unapereka kukongola kwako kwa anthu odutsawo.
15 ‘Koma unayamba kudalira kukongola kwako+ ndipo unakhala hule chifukwa cha kutchuka kwako.+ Unayamba kuchita uhule mosadziletsa ndi munthu aliyense wodutsa mʼnjira+ ndipo unapereka kukongola kwako kwa anthu odutsawo.