Ezekieli 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Unatenga zovala zako zina za mitundu yosiyanasiyana nʼkukongoletsera malo okwezeka pamene unkachitirapo uhule.+ Zinthu zimene siziyenera kuchitika ndipo zisadzachitikenso.
16 Unatenga zovala zako zina za mitundu yosiyanasiyana nʼkukongoletsera malo okwezeka pamene unkachitirapo uhule.+ Zinthu zimene siziyenera kuchitika ndipo zisadzachitikenso.