Ezekieli 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Unatenganso zinthu zako zodzikongoletsera zagolide ndi zasiliva zimene ndinakupatsa ndipo unapangira zifaniziro za munthu wamwamuna nʼkumachita nazo uhule.+
17 Unatenganso zinthu zako zodzikongoletsera zagolide ndi zasiliva zimene ndinakupatsa ndipo unapangira zifaniziro za munthu wamwamuna nʼkumachita nazo uhule.+