Ezekieli 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Unatenga zovala zako za nsalu yopeta nʼkuphimbira zifanizirozo ndipo unapereka mafuta anga ndi zonunkhiritsa zanga kwa zifanizirozo.+
18 Unatenga zovala zako za nsalu yopeta nʼkuphimbira zifanizirozo ndipo unapereka mafuta anga ndi zonunkhiritsa zanga kwa zifanizirozo.+