Ezekieli 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komanso buledi amene ndinakupatsa kuti udye, wopangidwa ndi ufa wosalala, mafuta ndi uchi, unamuperekanso kwa zifanizirozo kuti zikhale kafungo kosangalatsa.*+ Izi ndi zimene zinachitikadi,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
19 Komanso buledi amene ndinakupatsa kuti udye, wopangidwa ndi ufa wosalala, mafuta ndi uchi, unamuperekanso kwa zifanizirozo kuti zikhale kafungo kosangalatsa.*+ Izi ndi zimene zinachitikadi,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.