Ezekieli 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ‘Unatenga ana ako aamuna ndi aakazi amene unandiberekera+ nʼkuwapereka nsembe kwa mafano.+ Kodi zochita zako zauhulezo sizinakukwanire?
20 ‘Unatenga ana ako aamuna ndi aakazi amene unandiberekera+ nʼkuwapereka nsembe kwa mafano.+ Kodi zochita zako zauhulezo sizinakukwanire?