-
Ezekieli 16:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Pamene unkachita zinthu zako zonse zonyansa komanso zauhulezo, sunakumbukire zimene ndinakuchitira uli wakhanda pamene unali wamaliseche komanso wosavala, ukuponyaponya timiyendo tako mʼmwamba ndiponso uli magazi okhaokha.
-