Ezekieli 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Unamanga malo ako okwerawo pamalo oonekera bwino kwambiri mumsewu uliwonse ndipo kukongola kwako unakusandutsa chinthu chonyansa podzipereka kwa munthu* aliyense wodutsa+ ndipo unachulukitsa zochita zako zauhulezo.+
25 Unamanga malo ako okwerawo pamalo oonekera bwino kwambiri mumsewu uliwonse ndipo kukongola kwako unakusandutsa chinthu chonyansa podzipereka kwa munthu* aliyense wodutsa+ ndipo unachulukitsa zochita zako zauhulezo.+