Ezekieli 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Unachita uhule ndi ana aamuna a Iguputo,+ anthu oyandikana nawo amene ali ndi chilakolako champhamvu chogonana,* ndipo unandikhumudwitsa ndi zochita zako zauhule zosawerengeka.
26 Unachita uhule ndi ana aamuna a Iguputo,+ anthu oyandikana nawo amene ali ndi chilakolako champhamvu chogonana,* ndipo unandikhumudwitsa ndi zochita zako zauhule zosawerengeka.