Ezekieli 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chifukwa chosakhutira, unachitanso uhule ndi ana aamuna a Asuri.+ Koma utachita uhule ndi amuna amenewa sunakhutirebe.
28 Chifukwa chosakhutira, unachitanso uhule ndi ana aamuna a Asuri.+ Koma utachita uhule ndi amuna amenewa sunakhutirebe.