Ezekieli 16:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho unawonjezera kuchita zauhule ndi dziko la anthu a malonda* ndiponso Akasidi.+ Koma ngakhale unachita zimenezo sunakhutirebe.
29 Choncho unawonjezera kuchita zauhule ndi dziko la anthu a malonda* ndiponso Akasidi.+ Koma ngakhale unachita zimenezo sunakhutirebe.