Ezekieli 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Anthu amapereka mphatso kwa mahule onse,+ koma iweyo ndi amene wapereka mphatso kwa zibwenzi zako zonse.+ Umawapatsa ziphuphu kuti abwere kwa iwe kuchokera kumalo onse ozungulira kuti adzachite nawe zauhule.+
33 Anthu amapereka mphatso kwa mahule onse,+ koma iweyo ndi amene wapereka mphatso kwa zibwenzi zako zonse.+ Umawapatsa ziphuphu kuti abwere kwa iwe kuchokera kumalo onse ozungulira kuti adzachite nawe zauhule.+