Ezekieli 16:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndidzakupatsa chiweruzo chimene chimayenera kuperekedwa kwa akazi achigololo+ ndi kwa akazi okhetsa magazi+ ndipo magazi ako adzakhetsedwa mokwiya komanso mwansanje.+
38 Ndidzakupatsa chiweruzo chimene chimayenera kuperekedwa kwa akazi achigololo+ ndi kwa akazi okhetsa magazi+ ndipo magazi ako adzakhetsedwa mokwiya komanso mwansanje.+