Ezekieli 16:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Adzakubweretsera chigulu cha anthu+ kuti chikuukire. Iwo adzakugenda ndi miyala+ ndipo adzakupha ndi malupanga awo.+
40 Adzakubweretsera chigulu cha anthu+ kuti chikuukire. Iwo adzakugenda ndi miyala+ ndipo adzakupha ndi malupanga awo.+