Ezekieli 16:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Mkwiyo wanga ndidzauthetsera pa iwe+ moti sindidzakukwiyiranso.+ Ndidzangokhala osachita kalikonse ndipo sindidzakhalanso wokwiya.’
42 Mkwiyo wanga ndidzauthetsera pa iwe+ moti sindidzakukwiyiranso.+ Ndidzangokhala osachita kalikonse ndipo sindidzakhalanso wokwiya.’