Ezekieli 16:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Iweyo uli ngati mayi ako, amene ankanyansidwa ndi mwamuna wawo komanso ana awo. Ulinso ngati azichemwali ako amene ankanyansidwa ndi amuna awo ndi ana awo. Mayi ako anali Muhiti ndipo bambo ako anali a Chiamori.+
45 Iweyo uli ngati mayi ako, amene ankanyansidwa ndi mwamuna wawo komanso ana awo. Ulinso ngati azichemwali ako amene ankanyansidwa ndi amuna awo ndi ana awo. Mayi ako anali Muhiti ndipo bambo ako anali a Chiamori.+