Ezekieli 16:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Iwe sikuti unangoyenda mʼnjira zawo ndiponso sikuti unkangotsatira zinthu zawo zonyansa zimene ankachita basi, koma mʼkanthawi kochepa zochita zako zonse zinakhala zoipa kwambiri kuposa zimene iwowo ankachita.+
47 Iwe sikuti unangoyenda mʼnjira zawo ndiponso sikuti unkangotsatira zinthu zawo zonyansa zimene ankachita basi, koma mʼkanthawi kochepa zochita zako zonse zinakhala zoipa kwambiri kuposa zimene iwowo ankachita.+