-
Ezekieli 16:48Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
48 Pali ine Mulungu wamoyo, mchemwali wako Sodomu ndi ana ake aakazi, sanachite zofanana ndi zimene iwe ndi ana ako aakazi mwachita,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
-