Ezekieli 16:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 ‘Tamvera! Zolakwa za mchemwali wako Sodomu zinali izi: Iye ndi ana ake aakazi+ anali onyada,+ anali ndi chakudya chochuluka+ komanso ankakhala moyo wabata ndi wosatekeseka,+ koma sankathandiza anthu ovutika ndi osauka.+
49 ‘Tamvera! Zolakwa za mchemwali wako Sodomu zinali izi: Iye ndi ana ake aakazi+ anali onyada,+ anali ndi chakudya chochuluka+ komanso ankakhala moyo wabata ndi wosatekeseka,+ koma sankathandiza anthu ovutika ndi osauka.+