Ezekieli 16:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Koma ine ndidzakumbukira pangano limene ndinapangana nawe uli wakhanda ndipo ndidzachita nawe pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:60 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 17
60 Koma ine ndidzakumbukira pangano limene ndinapangana nawe uli wakhanda ndipo ndidzachita nawe pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale.+