Ezekieli 16:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Udzakumbukira khalidwe lako ndipo udzachita manyazi+ ukadzalandira azichemwali ako omwe ndi akulu ako komanso angʼono ako. Ndidzawapereka kwa iwe kuti akhale ana ako aakazi, koma osati chifukwa cha pangano limene ndinachita ndi iwe.
61 Udzakumbukira khalidwe lako ndipo udzachita manyazi+ ukadzalandira azichemwali ako omwe ndi akulu ako komanso angʼono ako. Ndidzawapereka kwa iwe kuti akhale ana ako aakazi, koma osati chifukwa cha pangano limene ndinachita ndi iwe.