Ezekieli 16:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Kenako udzakumbukira ndipo udzachita manyazi kwambiri moti sudzatha kutsegula pakamwa pako chifukwa cha manyaziwo,+ ndikadzaphimba machimo ako ngakhale kuti unachita zonsezi,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
63 Kenako udzakumbukira ndipo udzachita manyazi kwambiri moti sudzatha kutsegula pakamwa pako chifukwa cha manyaziwo,+ ndikadzaphimba machimo ako ngakhale kuti unachita zonsezi,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”