-
Ezekieli 17:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndiyeno unene kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Kodi mtengo umenewu zinthu zidzauyendera bwino? Kodi munthu wina sadzadula mizu yake+ nʼkuchititsa kuti zipatso zake ziwole komanso kuchititsa kuti mphukira zake zinyale?+ Mtengowo udzauma kwambiri moti sipadzachita kufunika dzanja lamphamvu kapena anthu ambiri kuti auzule ndi mizu yomwe.
-