-
Ezekieli 17:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ngakhale kuti mtengowo anautenga pamalo ena nʼkukaudzala pamalo ena, kodi zinthu zidzauyendera bwino? Kodi sudzaumiratu ukadzawombedwa ndi mphepo yakumʼmawa? Mtengowo udzauma pamalo amene unadzalidwapo.”’”
-