Ezekieli 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuwonjezera apo, inatenga mmodzi mwa ana* achifumu+ nʼkuchita naye pangano ndi kumulumbiritsa.+ Kenako mfumuyo inatenga anthu otchuka amʼdzikolo nʼkupita nawo kwawo+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:13 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 17
13 Kuwonjezera apo, inatenga mmodzi mwa ana* achifumu+ nʼkuchita naye pangano ndi kumulumbiritsa.+ Kenako mfumuyo inatenga anthu otchuka amʼdzikolo nʼkupita nawo kwawo+