Ezekieli 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 nʼcholinga choti ufumuwo ukhale waungʼono, usakhalenso wamphamvu, koma kuti ufumuwo udzapitirize kukhalapo ngati Aisiraeli atasunga pangano limene anachita.+
14 nʼcholinga choti ufumuwo ukhale waungʼono, usakhalenso wamphamvu, koma kuti ufumuwo udzapitirize kukhalapo ngati Aisiraeli atasunga pangano limene anachita.+