15 Koma kenako mfumu ya Yuda inapandukira mfumu ya Babulo+ potumiza amithenga ku Iguputo kuti akatenge mahatchi+ ndi gulu lalikulu la asilikali.+ Kodi zinthu zidzaiyendera bwino? Kodi munthu amene akuchita zinthu zimenezi angapewe chilango? Kodi angaphwanye pangano nʼkupewabe chilango?’+