Ezekieli 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, “Pali ine Mulungu wamoyo, munthu amene ananyoza lumbiro ndi kuphwanya pangano limene anachita ndi mfumu* imene inamulonga* ufumu, adzafera mʼdziko la Babulo, kumene mfumuyo imakhala.+
16 ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, “Pali ine Mulungu wamoyo, munthu amene ananyoza lumbiro ndi kuphwanya pangano limene anachita ndi mfumu* imene inamulonga* ufumu, adzafera mʼdziko la Babulo, kumene mfumuyo imakhala.+