Ezekieli 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Gulu lalikulu la asilikali komanso asilikali ambirimbiri a Farao sadzamuthandiza pankhondo,+ adani akadzamanga malo okwera omenyerapo nkhondo ndiponso mpanda womenyerapo nkhondo nʼcholinga chakuti aphe anthu ambiri.
17 Gulu lalikulu la asilikali komanso asilikali ambirimbiri a Farao sadzamuthandiza pankhondo,+ adani akadzamanga malo okwera omenyerapo nkhondo ndiponso mpanda womenyerapo nkhondo nʼcholinga chakuti aphe anthu ambiri.