Ezekieli 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye wanyoza lumbiro limenelo komanso waphwanya pangano. Ngakhale kuti analonjeza,* iye wachita zinthu zonsezi ndipo sadzapulumuka.”’
18 Iye wanyoza lumbiro limenelo komanso waphwanya pangano. Ngakhale kuti analonjeza,* iye wachita zinthu zonsezi ndipo sadzapulumuka.”’