Ezekieli 17:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndidzamuponyera ukonde wanga ndipo adzakodwa mu ukonde wanga wosakira.+ Ndiyeno ndidzamubweretsa ku Babulo nʼkumuweruza chifukwa chondichitira zinthu mosakhulupirika.+
20 Ndidzamuponyera ukonde wanga ndipo adzakodwa mu ukonde wanga wosakira.+ Ndiyeno ndidzamubweretsa ku Babulo nʼkumuweruza chifukwa chondichitira zinthu mosakhulupirika.+