Ezekieli 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Asilikali ake onse amene anathawa adzaphedwa ndi lupanga ndipo amene adzapulumuke adzabalalikira kumbali zonse.*+ Zikadzatero mudzadziwa kuti ine Yehova ndi amene ndanena zimenezi.”’+
21 Asilikali ake onse amene anathawa adzaphedwa ndi lupanga ndipo amene adzapulumuke adzabalalikira kumbali zonse.*+ Zikadzatero mudzadziwa kuti ine Yehova ndi amene ndanena zimenezi.”’+