Ezekieli 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndidzathyola nsonga yapamwamba penipeni pa mtengo wa mkungudza+ nʼkuidzala. Ndidzabudula mphukira yanthete pamwamba pa nsonga zake+ ndipo ndidzaidzala pamwamba pa phiri lalitali kwambiri.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:22 Nsanja ya Olonda,7/1/2007, ptsa. 12-139/15/1988, tsa. 18
22 ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndidzathyola nsonga yapamwamba penipeni pa mtengo wa mkungudza+ nʼkuidzala. Ndidzabudula mphukira yanthete pamwamba pa nsonga zake+ ndipo ndidzaidzala pamwamba pa phiri lalitali kwambiri.+