-
Ezekieli 17:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ndidzaidzala pamwamba pa phiri lalitali la ku Isiraeli. Nthambi zake zidzakula ndipo udzabereka zipatso nʼkukhala mtengo waukulu wa mkungudza. Mbalame zamitundu yonse zizidzakhala pansi pa mtengowo ndi mumthunzi wa masamba ake.
-