Ezekieli 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mitengo yonse yamʼthengo idzadziwa kuti ine Yehova ndatsitsa mtengo waukulu nʼkukweza mtengo wonyozeka.+ Idzadziwa kuti ndaumitsa mtengo wauwisi nʼkuchititsa maluwa mtengo umene unali wouma.+ Ine Yehova ndanena komanso kuchita zimenezi.”’”
24 Mitengo yonse yamʼthengo idzadziwa kuti ine Yehova ndatsitsa mtengo waukulu nʼkukweza mtengo wonyozeka.+ Idzadziwa kuti ndaumitsa mtengo wauwisi nʼkuchititsa maluwa mtengo umene unali wouma.+ Ine Yehova ndanena komanso kuchita zimenezi.”’”