Ezekieli 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kodi mwambi umene mumanena mʼdziko la Isiraeli wakuti, ‘Bambo adya mphesa zosapsa koma mano a ana ndi amene ayezimira,’+ umatanthauza chiyani? Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:2 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 18
2 “Kodi mwambi umene mumanena mʼdziko la Isiraeli wakuti, ‘Bambo adya mphesa zosapsa koma mano a ana ndi amene ayezimira,’+ umatanthauza chiyani?