Ezekieli 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani! Miyoyo yonse ndi yanga. Moyo wa bambo komanso moyo wa mwana, yonse ndi yanga. Moyo umene wachimwa ndi umene udzafe.* Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:4 Nsanja ya Olonda,10/1/1997, tsa. 199/15/1988, tsa. 18 Kukambitsirana, ptsa. 321-322
4 Tamverani! Miyoyo yonse ndi yanga. Moyo wa bambo komanso moyo wa mwana, yonse ndi yanga. Moyo umene wachimwa ndi umene udzafe.*