Ezekieli 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Sazunza munthu aliyense+ koma amabweza chikole kwa munthu amene anakongola zinthu zake.+ Salanda zinthu za ena mwauchifwamba+ koma amapereka chakudya chake kwa munthu amene ali ndi njala+ ndiponso amaphimba munthu wamaliseche ndi chovala.+
7 Sazunza munthu aliyense+ koma amabweza chikole kwa munthu amene anakongola zinthu zake.+ Salanda zinthu za ena mwauchifwamba+ koma amapereka chakudya chake kwa munthu amene ali ndi njala+ ndiponso amaphimba munthu wamaliseche ndi chovala.+