Ezekieli 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye sauza anthu kuti amupatse chiwongoladzanja akabwereketsa zinthu ndipo sakongoza zinthu mwa katapira+ koma amapewa kuchita zinthu mopanda chilungamo.+ Iye amatsatira chilungamo chenicheni akamaweruza munthu ndi mnzake.+
8 Iye sauza anthu kuti amupatse chiwongoladzanja akabwereketsa zinthu ndipo sakongoza zinthu mwa katapira+ koma amapewa kuchita zinthu mopanda chilungamo.+ Iye amatsatira chilungamo chenicheni akamaweruza munthu ndi mnzake.+