Ezekieli 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo amapitiriza kuyenda motsatira malamulo anga ndi kusunga zigamulo zanga kuti azichita zinthu mokhulupirika. Munthu ameneyu ndi wolungama, ndithu adzapitiriza kukhala ndi moyo,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
9 Ndipo amapitiriza kuyenda motsatira malamulo anga ndi kusunga zigamulo zanga kuti azichita zinthu mokhulupirika. Munthu ameneyu ndi wolungama, ndithu adzapitiriza kukhala ndi moyo,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.