-
Ezekieli 18:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 (ngakhale kuti bamboyo sanachitepo chilichonse mwa zinthu zimenezi), ngati mwanayo amadya chakudya choperekedwa nsembe kwa mafano mʼmapiri ndipo amagona ndi mkazi wa mnzake,
-