Ezekieli 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ngati amazunza munthu wovutika ndi wosauka,+ ngati amalanda zinthu za ena mwauchifwamba, ngati sabweza chikole, ngati amadalira mafano onyansa,+ ngati amachita makhalidwe onyansa,+
12 ngati amazunza munthu wovutika ndi wosauka,+ ngati amalanda zinthu za ena mwauchifwamba, ngati sabweza chikole, ngati amadalira mafano onyansa,+ ngati amachita makhalidwe onyansa,+