Ezekieli 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ngati amakongoza zinthu zake mwa katapira ndipo amauza anthu kuti apereke chiwongoladzanja,+ ndiye kuti mwanayo sadzapitiriza kukhala ndi moyo. Chifukwa wachita zinthu zonyansa zonsezi, iye adzaphedwa ndithu. Magazi ake adzakhala pamutu pake.
13 ngati amakongoza zinthu zake mwa katapira ndipo amauza anthu kuti apereke chiwongoladzanja,+ ndiye kuti mwanayo sadzapitiriza kukhala ndi moyo. Chifukwa wachita zinthu zonyansa zonsezi, iye adzaphedwa ndithu. Magazi ake adzakhala pamutu pake.