-
Ezekieli 18:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Koma tiyerekeze kuti bambo ali ndi mwana wamwamuna amene amaona machimo onse amene bambo akewo amachita. Ngakhale kuti mwanayo amaona bambo ake akuchita machimowo, iye sachita nawo.
-