Ezekieli 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma ngati munthu woipa wasiya kuchita machimo ake onse amene ankachita ndipo akusunga malamulo anga nʼkumachita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo, ndithu iye adzapitiriza kukhala ndi moyo. Sadzafa ayi.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:21 Nsanja ya Olonda,7/1/2012, tsa. 18
21 Koma ngati munthu woipa wasiya kuchita machimo ake onse amene ankachita ndipo akusunga malamulo anga nʼkumachita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo, ndithu iye adzapitiriza kukhala ndi moyo. Sadzafa ayi.+