Ezekieli 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma inu mudzanena kuti: “Njira za Yehova nʼzopanda chilungamo.”+ Tamverani inu a nyumba ya Isiraeli. Kodi njira zanga nʼzimene zili zopanda chilungamo?+ Kodi njira zanu si zimene zili zopanda chilungamo?+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:25 Nsanja ya Olonda,10/15/2010, ptsa. 3-4
25 Koma inu mudzanena kuti: “Njira za Yehova nʼzopanda chilungamo.”+ Tamverani inu a nyumba ya Isiraeli. Kodi njira zanga nʼzimene zili zopanda chilungamo?+ Kodi njira zanu si zimene zili zopanda chilungamo?+