Ezekieli 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Munthu amene amachita zinthu zabwino akasiya kuchita zabwinozo nʼkumachita zoipa,* nʼkufa chifukwa cha zochita zakezo, adzakhala kuti wafa chifukwa cha zoipa zake.
26 Munthu amene amachita zinthu zabwino akasiya kuchita zabwinozo nʼkumachita zoipa,* nʼkufa chifukwa cha zochita zakezo, adzakhala kuti wafa chifukwa cha zoipa zake.