Ezekieli 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndipo ngati munthu woipa wasiya kuchita zinthu zoipa zimene ankachita nʼkuyamba kuchita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo, iye adzapulumutsa moyo wake.+
27 Ndipo ngati munthu woipa wasiya kuchita zinthu zoipa zimene ankachita nʼkuyamba kuchita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo, iye adzapulumutsa moyo wake.+