Ezekieli 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma nyumba ya Isiraeli idzanena kuti: “Njira za Yehova nʼzopanda chilungamo.” Kodi nʼzoona kuti njira zanga nʼzimene zili zopanda chilungamo, inu a nyumba ya Isiraeli?+ Kodi njira zanu si zimene zili zopanda chilungamo?’ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:29 Nsanja ya Olonda,8/15/2013, ptsa. 11-12
29 Koma nyumba ya Isiraeli idzanena kuti: “Njira za Yehova nʼzopanda chilungamo.” Kodi nʼzoona kuti njira zanga nʼzimene zili zopanda chilungamo, inu a nyumba ya Isiraeli?+ Kodi njira zanu si zimene zili zopanda chilungamo?’