Ezekieli 18:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 ‘Inetu sindisangalala ndi imfa ya munthu aliyense,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. ‘Choncho siyani kuchita zoipa kuti mupitirize kukhala ndi moyo.’”+
32 ‘Inetu sindisangalala ndi imfa ya munthu aliyense,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. ‘Choncho siyani kuchita zoipa kuti mupitirize kukhala ndi moyo.’”+